Chivumbulutso 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yohaneyo anachitira umboni mawu a Mulungu,+ ndiponso umboni umene Yesu Khristu anapereka,+ kutanthauza zonse zimene anaona. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 16-17
2 Yohaneyo anachitira umboni mawu a Mulungu,+ ndiponso umboni umene Yesu Khristu anapereka,+ kutanthauza zonse zimene anaona.