Chivumbulutso 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako ndinamva guwa lansembe likunena kuti: “Inde, Yehova Mulungu, inu Wamphamvuyonse,+ zigamulo zanu n’zoona ndi zolungama.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:7 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 224-225
7 Kenako ndinamva guwa lansembe likunena kuti: “Inde, Yehova Mulungu, inu Wamphamvuyonse,+ zigamulo zanu n’zoona ndi zolungama.”+