May Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya May 2020 Zimene Tinganene May 4-10 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 36-37 Yosefe Anachitiridwa Nsanje MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mwakonzekera? May 11-17 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 38-39 Yehova Sanasiye Yosefe MOYO WATHU WACHIKHRISTU Khalani Ngati Yosefe—Thawani Dama May 18-24 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 40-41 Yehova Anapulumutsa Yosefe May 25-31 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 42-43 Yosefe Anasonyeza Kudziletsa Kwambiri MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muziyesetsa Kumvetsa Nkhani Yonse