January Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya January 2018 Zitsanzo za Ulaliki January 1-7 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 1-3 “Ufumu Wakumwamba Wayandikira” January 8-14 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 4-5 Zimene Tikuphunzira pa Zomwe Yesu Anaphunzitsa pa Ulaliki Wapaphiri MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Tingatsatire Bwanji Malangizo Akuti Ukayanjane Ndi M’bale Wako Choyamba? January 15-21 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 6-7 Pitirizani Kufunafuna Ufumu Choyamba KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Musamade Nkhawa January 22-28 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 8-9 Yesu Ankakonda Anthu January 29–February 4 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 10-11 Yesu Ankatsitsimula Ena