Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 January tsamba 4
  • January 15-21

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 15-21
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 January tsamba 4

January 15-21

Mateyu 6-7

  • Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pitirizani Kufunafuna Ufumu Choyamba”: (10 min.)

    • Mat. 6:10​—Yesu anatchula Ufumu wa Mulungu koyambirira m’pemphero lachitsanzo, zomwe zikusonyeza kuti ndi wofunika kwambiri (bhs 178 ¶12)

    • Mat. 6:24​—N’zosatheka kumatumikira Mulungu ndi “chuma” nthawi imodzi (“Kapolo”mfundo zimene ndikuphunzira, pa Mat. 6:24, nwtsty)

    • Mat. 6:33​—Yehova amapereka zinthu zofunikira kwa atumiki ake okhulupirika omwe amaika zinthu zokhudza Ufumu pamalo oyamba (“pitirizani kufunafuna Ufumu” “chilungamo” ”chake” mfundo zimene ndikuphunzirapa Mat. 6:33, nwtsty; w16.07 12 ¶18)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mat. 7:12​—Kodi tingagwiritse ntchito bwanji vesili tikamakonzekera zoti tikalankhule mu utumiki? (w14 5/15 14-15 ¶14-16)

    • Mat. 7:28, 29​—Kodi anthu anakhudzidwa bwanji ndi zimene Yesu ankaphunzitsa ndipo n’chifukwa chiyani zinawakhudza choncho? (“linadabwa” kaphunzitsidwe kake “osati monga alembi awo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 5:28, 29, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 6:1-18

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulaliki. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulaliki. Munthu yemwe munacheza naye ulendo wapita simunamupeze pakhomo, ndiye mwakumana ndi wachibale wake.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri (Osapitirira 5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 118

  • “Musamade Nkhawa”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yakuti Zimene Tikuphunzira pa Mafanizo Amene Yesu Ananena​—Onetsetsani Mbalame ndi Maluwa.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 13 ¶1-10 komanso tsamba 132-133

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena