July Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya July 2018 Zimene Tinganene July 2-8 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 6-7 Muzikhala Owolowa Manja July 9-15 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 8-9 Kodi Chofunika N’chiyani Kuti Munthu Akhale Wotsatira wa Yesu? July 16-22 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 10-11 Fanizo la Msamariya Wachifundo MOYO WATHU WACHIKHRISTU N’chifukwa Chiyani Sitiyenera Kulowerera Ndale? (Mika 4:2) July 23-29 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 12-13 “Ndinu Ofunika Kwambiri Kuposa Mpheta Zambiri” July 30–August 5 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 14-16 Fanizo la Mwana Wolowerera MOYO WATHU WACHIKHRISTU Mwana Wolowerera