November Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya November 2019 Zimene Tinganene November 4-10 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 YOHANE 1-5 Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko MOYO WATHU WACHIKHRISTU Musamatengere Maganizo a M’dzikoli Mukamakonzekera Ukwati November 11-17 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 YOHANE 1-13; 3 YOHANE 1-14–YUDA 1-25 Tiyenera Kuchita Khama Kuti Tikhalebe m’Choonadi November 18-24 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 1-3 “Ndikudziwa Ntchito Zako” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yehova Amadziwa Zimene Timafunikira November 25–December 1 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 4-6 Anthu 4 Okwera Pamahatchi MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yehova Amakonda Munthu Wopereka Mokondwera