Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 April tsamba 5
  • Yobu Ndi Chitsanzo Chabwino pa Nkhani ya Kukhala ndi Mtima Wosagawanika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yobu Ndi Chitsanzo Chabwino pa Nkhani ya Kukhala ndi Mtima Wosagawanika
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Yobu Analemekeza Dzina la Yehova
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Mfundo Zazikulu za M’buku la Yobu
    Nsanja ya Olonda—2006
  • Tidzayenda Mogwirizana Ndi Mtima Wathu Wosagawanika
    Nsanja ya Olonda—2010
  • Yobu Anakhalabe Wokhulupirika Pamene Ankayesedwa
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 April tsamba 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOBU 28-32

Yobu Ndi Chitsanzo Chabwino pa Nkhani ya Kukhala ndi Mtima Wosagawanika

Yobu ankatsatira mfundo za makhalidwe abwino za Yehova ndi mtima wonse

31:1

  • Iye ankakonda kwambiri mkazi wake ndipo sanalole kuti maso ake aziyang’ananitsitsa akazi ena mowalakalaka

    Yobu ndi mkazi wake

Yobu ndi chitsanzo chabwino pa nkhani ya kukhala bwino ndi ena

31:13-15

  • Anali wodzichepetsa, wachilungamo ndiponso wachifundo. Ankakonda anthu onse, olemera ndi osauka omwe

    Yobu akuyankhula ndi mnyamata

Yobu anali woolowa manja ndiponso sanali wodzikonda

31:16-19

  • Ankathandiza anthu ovutika

    Yobu akupereka mphesa kwa mwana wamng’ono
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena