Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 August tsamba 4
  • Muzikhala ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo​—Kulimba Mtima

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzikhala ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo​—Kulimba Mtima
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Kukhala Olimba Mtima Sikovuta Kwambiri
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • ‘Limba Mtima Ndipo Ugwire Ntchitoyi’
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • Khalani Olimba Mtima!
    Nsanja ya Olonda—1993
  • Ndithandizeni Ndikhale Wolimba Mtima
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 August tsamba 4

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzikhala ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo​—Kulimba Mtima

N’CHIFUKWA CHIYANI KULIMBA MTIMA N’KOFUNIKA?

  • Kulalikira kumafuna kulimba mtima.​—Mac. 5:27-29, 41, 42

  • Pa chisautso chachikulu tidzafunika kukhala olimba mtima.​—Mat. 24:15-21

  • Kuopa anthu kumabweretsa mavuto.​—Yer. 38:17-20; 39:4-7

KODI TINGASONYEZE BWANJI KULIMBA MTIMA?

  • Tiziganizira zimene Yehova anachita populumutsa anthu.​—Eks. 14:13

  • Tizipemphera kuti Mulungu atithandize kukhala olimba mtima.​—Mac. 4:29, 31

  • Tizidalira Yehova.​—Sal. 118:6

Abale awiri akulimbikitsa m’bale wina kuti akalalikire nawo m’malo opezeka anthu ambiri

Kodi ndiyenera kulimbana ndi zinthu ziti zimene zimandichititsa mantha ndikamatumikira Mulungu?

ONERANI VIDIYO YAKUTI MUZIPEWA ZINTHU ZIMENE ZINGAWONONGE KHALIDWE LANU LA KUKHULUPIRIKA—KUOPA ANTHU, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • N’chifukwa chiyani kulimba mtima n’kofunika tikakhala mu utumiki?

  • Kodi lemba la Miyambo 29:25 likusonyeza bwanji kusiyana pakati pa kuopa anthu ndi kukhulupirira Yehova?

  • Kodi n’chifukwa chiyani tiyenera kukhala olimba mtima panopa?

CHITSANZO CHA M’BAIBULO CHOFUNIKA KUCHIGANIZIRA:

Ezekieli ankadziwa kuti adzakumana ndi mavuto pa ntchito yake yauneneri.​—Ezek. 2:3-7; 33:7-9.

Dzifunseni kuti, ‘Kodi ndingatsanzire bwanji Ezekieli pa nkhani ya kulimba mtima?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena