Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 February tsamba 3
  • Khristu Anavutika Chifukwa cha Ife

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Khristu Anavutika Chifukwa cha Ife
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Mtumiki wa Yehova “Analasidwa Chifukwa cha Zolakwa Zathu”
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga
    Nsanja ya Olonda—2000
  • Zisonyezero Ziŵiri Zazikulu Kwambiri za Chikondi Zomwe Sizinapangidwepo ndi Kale Lonse
    Nsanja ya Olonda—1987
  • Kupambana Chiyeso cha Kukhulupirika
    Nsanja ya Olonda—1996
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 February tsamba 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 52-57

Khristu Anavutika Chifukwa cha Ife

“Iye ananyozedwa ndipo anthu anali kumupewa. . . . Ifeyo tinamuona ngati wosautsidwa, wokwapulidwa ndi Mulungu, ndiponso wozunzidwa”

53:3-5

  • Yesu ankanyozedwa ndiponso kunamiziridwa kuti ndi wonyoza Mulungu. Anthu ena ankakhulupirira kuti Mulungu ndi amene ankamusautsa kapena kuti kumulanga

    Yesu sanasiye kukhala wokhulupirika ngakhale kuti ankadziwa kuti adzavutika

“Zinamukomera Yehova kuti mtumiki wake aphwanyidwe . . . ndipo ndi dzanja lake, adzakwaniritsa zokonda Yehova.”

53:10

  • N’zosachita kufunsa kuti Yehova anavutika kwambiri ataona mwana wake akuphedwa. Komabe anasangalala chifukwa chakuti Yesu sanasiye kukhala wokhulupirika. Yesu anakhala wokhulupirika mpaka imfa ndipo izi zinathandiza kutsutsa zimene Satana ananena zoti atumiki a Mulungu sangakhale okhulupirika atakumana ndi mavuto. Zinachititsanso kuti anthu olapa apeze madalitso. Choncho imfa yakeyi inathandiza kukwaniritsa zimene Yehova ankafuna

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena