Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 October tsamba 8
  • “Ana Anu Aamuna ndi Ana Anu Aakazi Adzanenera”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Ana Anu Aamuna ndi Ana Anu Aakazi Adzanenera”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Chenjerani ndi Aneneri Onyenga!
    Nsanja ya Olonda—1992
  • Tipita Nanu Limodzi
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2020
  • Kodi ‘Adzapulumuka Ndani’?
    Nsanja ya Olonda—1998
  • Dzina la Mulungu
    Galamukani!—2017
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 October tsamba 8

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOWELI 1-3

“Ana Anu Aamuna ndi Ana Anu Aakazi Adzanenera”

2:28, 29

Akhristu odzozedwa amagwira ntchito yonenera. Iwo amauza ena za “zinthu zazikulu za Mulungu” ndipo amalengeza “uthenga wabwino wa Ufumu.” (Mac. 2:11, 17-21; Mat. 24:14) Ankhosa zina amathandiza odzodzedwawa pogwira nawo ntchito yolalikira.

Akhristu odzozedwa akugwira ntchito yonenera polalikira “uthenga wabwino wa Ufumu” kwa anthu amitundu yosiyanasiyana pa tsiku la pentekosite

2:32

Kodi ‘kuitana pa dzina la Yehova’ kumatanthauza chiyani?

  • Kudziwa dzinalo

  • Kulemekeza dzinalo

  • Kudalira komanso kukhulupirira mwiniwake wa dzinalo

Dzifunseni kuti, ‘Kodi ndingathandize bwanji Akhristu odzozedwa omwe amagwira ntchito yonenera?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena