Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 49
  • Tizisangalatsa Mtima wa Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tizisangalatsa Mtima wa Yehova
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Tikondweretse Mtima wa Yehova
    Imbirani Yehova
  • Kukondweretsa Mtima wa Yehova
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Ana Amene Amakondwereta Mtima wa Yehova
    Nsanja ya Olonda—1987
  • ‘Kondwerani, Anthu Inu’!
    Imbirani Yehova Zitamando
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 49

NYIMBO 49

Tizisangalatsa Mtima wa Yehova

Losindikizidwa

(Miyambo 27:11)

  1. 1. M’lungu takulonjezani

    Kuchita zofuna zanu.

    Tizigwira ntchito yanu,

    Tizikusangalatsani.

  2. 2. Kapolo wanu wanzeru

    Amalengeza za inu.

    Amatipatsa chakudya

    Kuti tizikumverani.

  3. 3. Mutipatse mzimu wanu

    Kuti tikhulupirike

    Ndipo makhalidwe athu

    Azikusangalatsani.

(Onaninso Mat. 24:​45-47; Luka 11:13; 22:42.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena