Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 3
  • “Mulungu Ndiye Chikondi”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Mulungu Ndiye Chikondi”
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • “Mulungu Ndi Chikondi”
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tanthauzo la Kukonda Mnansi Wathu
    Nsanja ya Olonda—2006
  • “Pitirizani Kusonyeza Chikondi”
    Yandikirani Yehova
  • Kondani Mulungu Amene Amakukondani
    Nsanja ya Olonda—2006
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 3

Nyimbo 3

“Mulungu Ndiye Chikondi”

Losindikizidwa

(1 Yohane 4:7, 8)

1. Mulungu ndiye chikondi,

Wati: ‘Yendani nane.’

Pokonda M’lungu ndi mnansi,

Tizichita zabwino.

Tikatero tidzakondwa;

Tidzapezanso moyo.

Tiyenitu tisonyeze

Chikondi ngati Khristu.

2. Chikondi chimathandiza

Kuchita zabwinodi.

Tikalakwa, amatithandiza

kupeza mphamvu.

Chikondi chilibe nsanje

Koma chimapirira.

Tikamakonda abale,

Tidzadalitsidwadi.

3. Musalole kuti mkwiyo

Ukutsogolereni.

Khulupirirani M’lungu;

Adzakuphunzitsani

Kukonda M’lungu ndi mnansi,

Chikondi chenicheni.

Tizisonyeza anzathu

Chikondi cha Mulungu.

(Onaninso Maliko 12:30, 31; 1 Akor. 12:31–13:8; 1 Yoh. 3:23.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena