Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 26
  • Yendani ndi Mulungu!

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yendani ndi Mulungu!
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • O Yendani ndi Mulungu!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Muziyenda Ndi Mulungu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tiziphunzitsidwa
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tiziphunzitsidwa Ndi Yehova
    Imbirani Yehova
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 26

Nyimbo 26

Yendani ndi Mulungu!

Losindikizidwa

(Mika 6:8)

1. Yendanitu ndi Mulungu;

Kondani chifundo.

Khulupirirani M’lungu;

Kuti musatope.

Mukatsatabe cho’nadi,

Simudzanyengedwa;

Azikutsogolerani

Yehova Mulungu.

2. Yendanitu mu chiyero

Musachite tchimo.

Kulaninso mwauzimu,

Yehova akondwe.

Pazinthu zonse zoyera

Ndiponso zoona,

Ganizirani zonsezi,

Dalirani M’lungu.

3. Yendanitu mowongoka,

Mudzapeza phindu.

Mudzakhala okhutira,

Zomwe ndi dalitso.

Yendanitu ndi Mulungu,

M’tamandeni ndithu.

Tidzapezatu chimwemwe,

Mu ’tumiki wake.

(Onaninso Gen. 5:24; 6:9; Afil. 4:8; 1 Tim. 6:6-8.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena