Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 September tsamba 3
  • Kulambira Koyera Kunabwezeretsedwa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kulambira Koyera Kunabwezeretsedwa
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • “Ili ndi Lamulo Lokhudza Kachisi”
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • ‘Ufotokoze za Kachisiyu’
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • ‘Ika Mtima Wako pa’ Kachisi wa Mulungu!
    Nsanja ya Olonda—1999
  • Mmene Masomphenya a Ezekieli Onena za Kachisi Akutikhudzira
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 September tsamba 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 42-45

Kulambira Koyera Kunabwezeretsedwa

Masomphenya a Ezekieli okhudza kachisi anatsimikizira Ayuda okhulupirika omwe anali ku ukapolo kuti kulambira koyera kudzabwezeretsedwa. Komanso anawakumbutsa mfundo zapamwamba za Yehova zokhudza kulambira koyera.

Wansembe akuphunzitsa Chilamulo kwa Aisiraeli omwe asonkhana ndipo mkulu akuphunzitsa mfundo zochokera m’Baibulo pamsonkhano wa mpingo

Ansembe ankayenera kuphunzitsa anthu mfundo za Yehova

44:23

Fotokozani zitsanzo zosonyeza mmene kapolo wokhulupirika ndi wanzeru watithandizira kuti tizidziwa kusiyana pakati pa chinthu chodetsa ndi choyera. (kr 110-117)

Anthu ankathandiza atsogoleri awo

45:16

Kodi tingathandize akulu mumpingo m’njira ziti?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena