September 4-10
Ezekieli 42-45
Nyimbo Na. 26 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kulambira Koyera Kunabwezeretsedwa”: (10 min.)
Ezek. 43:10-12—Masomphenya a Ezekieli okhudza kachisi anathandiza Ayuda omwe anali ku ukapolo kuti alape komanso anawatsimikizira kuti kulambira koyera kudzabwezeretsedwa pamalo ake okwezeka (w99 3/1 8 ¶3; it-2 1082 ¶2)
Ezek. 44:23—Ansembe ankafunika kuphunzitsa anthu kuti adziwe “kusiyana kwa chinthu chodetsedwa ndi choyera”
Ezek. 45:16—Anthu ankayenera kuthandiza atsogoleri amene Yehova anawasankha kuti aziwatsogolera (w99 3/1 10 ¶10)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Ezek. 43:8, 9—Kodi Aisiraeli anadetsa bwanji dzina la Mulungu? (it-2 467 ¶4)
Ezek. 45:9, 10—Kodi Yehova amafuna kuti anthu amene amamutumikira azichita chiyani nthawi zonse? (it-2 140)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 44:1-9
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Kukambirana “Zitsanzo za Ulaliki.” Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“N’chifukwa Chiyani Mumaona Kuti Kulambira Koyera N’kofunika?”: (15 min.) Nkhani yokambirana.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 6 ¶8-15 komanso tsamba 63
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 115 ndi Pemphero