Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsamba 3
  • Isaki Anapeza Mkazi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Isaki Anapeza Mkazi
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Abulahamu Anasonyeza Kuti Anali Wokhulupirika
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Umboni Waukulu Wakuti Mulungu Amatikonda
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Mulungu Ayesa Abrahamu
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
  • Isake Apeza Mkazi Wabwino
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 March tsamba 3
Rabeka ali ndi mtsuko waukulu wamadzi ndipo akuthira madziwo m’chomwera ziweto kuti ngamila zimwe. Mtumiki wa Abulahamu akungomuyang’ana ali chapatali.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 24

Isaki Anapeza Mkazi

24:2-4, 11-15, 58, 67

Mtumiki wa Abulahamu anapempha Yehova kuti amuthandize kusankha mkazi wa Isaki. (Ge 24:42-44) Nafenso tizipempha Yehova kuti atithandize kusankha zoyenera kuchita pa nkhani zikuluzikulu. Kodi tingachite bwanji zimenezi?

  • Tizipemphera

  • Tiziwerenga Mawu a Mulungu komanso tizifufuza m’mabuku athu

  • Tizipempha abale ndi alongo olimba mwauzimu kuti atithandize nzeru

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena