Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 9
  • Musamatsanzire Anthu Amene Ndi Osakhulupirika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Musamatsanzire Anthu Amene Ndi Osakhulupirika
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Kupambana Chiyeso cha Kukhulupirika
    Nsanja ya Olonda—1996
  • ‘Inu Nokha Ndinu Wokhulupirika’
    Yandikirani Yehova
  • Kutumikira Limodzi ndi Gulu la Yehova Mokhulupirika
    Nsanja ya Olonda—1997
  • Taonani Okhulupirika!
    Nsanja ya Olonda—1996
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 9
Nthaka ikung’ambika ndipo ikumeza Aisiraeli ogalukira.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Musamatsanzire Anthu Amene Ndi Osakhulupirika

Kora, Datani ndi Abiramu anasonyeza kusamvera Yehova pogalukira dongosolo lake. Yehova anawononga anthuwa komanso ena amene anali kumbali yawo. (Nu 16:26, 27, 31-33) Kodi ndi zochitika ziti zimene zingayese kukhulupirika kwathu kwa Yehova? Kodi ndi zitsanzo ziti za m’Baibulo zimene zingatithandize kuti tisamatsanzire anthu osakhulupirika?

ONERANI VIDIYO YAKUTI MUSAMATSANZIRE ANTHU OSAKHULUPIRIKA NDIPO KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Chithunzi cha muvidiyo yakuti ‘Musamatsanzire Anthu Osakhulupirika.’ Neliya akuona m’maganizo mwake mnyamata wina akumupatsa mowa kupate.

    Kodi Neliya anakumana ndi mayesero otani, nanga ndi chitsanzo chiti chimene chinamuthandiza kuti asonyeze kukhulupirika?

  • Chithunzi cha muvidiyo yakuti ‘Musamatsanzire Anthu Osakhulupirika.’ M’bale amene wakhumudwa akuganizira za nkhani imene yamukwiyitsa.

    Kodi m’bale wina amene anakhumudwa anakumana ndi mayesero otani, nanga ndi chitsanzo chiti chomwe chinamuthandiza kuti asonyeze kukhulupirika?

  • Chithunzi cha muvidiyo yakuti ‘Musamatsanzire Anthu Osakhulupirika.’ Eliyoti akuona m’maganizo mwake akulankhula ndi mlongo amene banja lake latha ali awiriwiri pamalo oimika magalimoto ku Nyumba ya Ufumu

    Kodi M’bale Eliyoti anakumana ndi mayesero otani, nanga ndi chitsanzo chiti chimene chinamuthandiza kuti asonyeze kukhulupirika?

  • Chithunzi cha muvidiyo yakuti ‘Musamatsanzire Anthu Osakhulupirika.’ M’bale wachinyamata akuyang’ana linki ya malo otchovera juga a pa intaneti imene wina wamutumizira pafoni yake.

    Kodi m’bale wina anakumana ndi mayesero otani kusukulu, nanga ndi chitsanzo chiti chimene chinamuthandiza kuti asonyeze kukhulupirika?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena