Woyang’anira dera ndi mkazi wake ku France, mu 1957
Zimene Tinganene
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi dzina la Mulungu ndi ndani?
Lemba: Sal. 83:18
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi timadziwa bwanji kuti Yehova Mulungu amafuna kuti tikhale anzake?
○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA
Funso: Kodi timadziwa bwanji kuti Yehova Mulungu amafuna kuti tikhale anzake?
Lemba: Yak. 4:8
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tingatani kuti tikhale anzake a Mulungu?
○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI
Funso: Kodi tingatani kuti tikhale anzake a Mulungu?
Lemba: Yoh. 17:3
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tingakhale bwanji anzake a Mulungu pomwe sitinayambe tamuonapo?