January 7-13
MACHITIDWE 21-22
Nyimbo Na. 55 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chifuniro cha Yehova Chichitike”: (10 min.)
Mac. 21:8-12—Akhristu anzake a Paulo anamupempha kuti asapite ku Yerusalemu chifukwa cha mavuto amene ankayembekezera kukakumana nawo kumeneko (bt 177-178 ¶15-16)
Mac. 21:13—Paulo anali wofunitsitsa kuchita zimene Yehova ankafuna (bt 178 ¶17)
Mac. 21:14—Abale ataona kuti Paulo watsimikiza mtima, anasiya kumuletsa (bt 178 ¶18)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Mac. 21:23, 24—N’chifukwa chiyani akulu a ku Yerusalemu anauza Paulo malangizo amenewa ngakhale kuti pa nthawiyi Akhristu sanalinso pansi pa Chilamulo cha Mose? (bt 184-185 ¶10-12)
Mac. 22:16—Kodi kubatizidwa kwa Paulo kunachotsa bwanji machimo ake? (“kusamba kuti uchotse machimo ako mwa kuitana pa dzina lake” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mac. 22:16, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mac. 21:1-19 (th phunziro 5)a
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Mawu Oyamba Abwino, kenako kambiranani mfundo za m’phunziro 1 m’kabuku ka Kuphunzitsa.
Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w10 2/1 13 ¶1 mpaka 14 ¶2—Mutu: Kodi Akhristu Ayenera Kusunga Sabata? (th phunziro 1)b
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Yehova Anatithandiza Kulera Ana Athu”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 20
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero