LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp20 na. 1 tsa. 16
  • Mmene Coonadi Cingakuthandizileni

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mmene Coonadi Cingakuthandizileni
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • KODI MUYENELA KUCITA CIANI?
  • Iye “Amakudelani Nkhawa”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
  • Kodi Munadzifunsapo?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
  • Mungakhale pa Ubwenzi na Mulungu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
  • Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?
    Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
wp20 na. 1 tsa. 16

Mmene Mungapindulile Mukadziŵa Coonadi

Mulungu amene sanganame, akukupatsani ciyembekezo ca “moyo wosatha.”​—Yohane 3:16.

KODI MUYENELA KUCITA CIANI?

Mtsikana aŵelenga Baibo pa tabuleti yake mu lesitalanti
  • Phunzilani Mawu a Mulungu, amene ni coonadi.—Yohane 17:3, 17.

  • Sankhani kumvela Mulungu. —Deuteronomo 30:19, 20.

  • Muziseŵenzetsa malangizo othandiza a Mulungu mu umoyo wanu.—Yakobo 1:25.

Mboni za Yehova pa dziko lonse lapansi zapindula cifukwa cophunzila coonadi ca m’Baibo. Iwo ni okonzeka kukuuzankoni zimene amaphunzila.

Kuti mudziŵe zambili zokhudza colinga ca Mulungu kwa anthu, onani nkhani 3 m’buku lakuti Zimene Baibulo Ingatiphunzitse, yolembewa na Mboni za Yehova. Ipezekanso pa webusaiti ya www.jw.org.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani