Abale okhulupilika atamasulidwa m’ndende yacibalo ku Germany mu 1945
Makambilano Acitsanzo
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi Mulungu amawaona bwanji anthu amene amamufuna-funa?
Lemba: 1 Pet. 5:6, 7
Ulalo: Kodi Mulungu amasamalila munthu aliyense payekha-payekha?
○●○ ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA
Funso: Kodi Mulungu amasamalila munthu aliyense payekha-payekha?
Lemba: Mat. 10:29-31
Ulalo: Tidziŵa bwanji kuti Mulungu amatimvetsetsa?
○○● ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI
Funso: Tidziŵa bwanji kuti Mulungu amatimvetsetsa?
Lemba: Sal. 139:1, 2, 4
Ulalo: Kodi timapindula bwanji na cisamalilo ca Mulungu?