LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 40
  • Pitirizani Kufuna Ufumu Choyamba

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pitirizani Kufuna Ufumu Choyamba
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Pitilizani Kufuna-funa Ufumu Coyamba
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nyimbo Yatsopano
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nyimbo Yatsopano
    Imbirani Yehova
  • Moyo Wosatha Watheka!
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 40

Nyimbo 40

Pitirizani Kufuna Ufumu Choyamba

(Mateyo 6:33)

1. Chomwe Yehova afuna,

Chomwe chim’sangalatsa,

Ndicho Ufumu wa Khristu,

Womwe ukonze zonse.

(KOLASI)

M’fune Ufumu choyamba

Ndi chilungamo chake.

M’tamande pa amitundu

Ndi kum’tumikirabe.

2. Musade nkhawa n’zamawa

Za chakudya ndi madzi.

M’lungu atisamalira

Tikafuna Ufumu.

(KOLASI)

M’fune Ufumu choyamba

Ndi chilungamo chake.

M’tamande pa amitundu

Ndi kum’tumikirabe.

3. Tsono lalika uthenga

Uthandize enanso

Azidalira Yehova

Ndi Ufumu wakewo.

(KOLASI)

M’fune Ufumu choyamba

Ndi chilungamo chake.

M’tamande pa amitundu

Ndi kum’tumikirabe.

(Onaninso Sal. 27:14; Mat. 6:34; 10:11, 13; 1 Pet. 1:21.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani