LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 15
  • Tamandani Woyamba Kubadwa wa Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tamandani Woyamba Kubadwa wa Yehova
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Tamandani Woyamba Kubadwa wa Yehova!
    Imbirani Yehova
  • Tamandani Yehova, Mulungu Wathu!
    Imbirani Yehova
  • Tamandani Yehova, Mulungu Wathu!
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Tamandani Mfumu Yatsopano Yodzalamulila Dziko
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 15

NYIMBO 15

Tamandani Woyamba Kubadwa wa Yehova

Yopulinta

(Aheberi 1:6)

  1. 1. Tamandani Yesu,

    Mfumu ya cilungamo.

    Ni Woyamba Kubadwa

    wa Atate Yehova.

    Adzayeletsa dzina

    la Atate wake.

    Adzaonetsa onse

    M’lungu ni Yehova.

    (KOLASI)

    Tamandani Yesu,

    Wodzozedwa wa M’lungu.

    Yehova ‘namusankha

    Iye lomba ni mfumu.

  2. 2. Tamandani Yesu,

    Iye anatifela

    Kuti ‘se tikakhale

    Na moyo wamuyaya.

    Ukwati wake Khristu

    Udzadziŵikitsa

    Ucifumu na mphamvu

    Za Yehova M’lungu.

    (KOLASI)

    Tamandani Yesu,

    Wodzozedwa wa M’lungu.

    Yehova ‘namusankha

    Iye lomba ni mfumu.

(Onaninso Sal. 2:6; 45:3, 4; Chiv 19:8.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani