Khalani Wolimba Mtima!
SALIMO 138:3
KUM’MAŴA
8:30 Nyimbo Zamalimba
8:40 Nyimbo Na. 73 na Pemphelo
8:50 Yehova Ndiye Amatilimbitsa Mtima
9:05 Yosiilana: Khalani Wolimba Mtima Monga . . .
Inoki
Mose
Yehosafati
Petulo
10:05 Nyimbo Na. 69 na Zilengezo
10:15 Khalani Wolimba Mtima mu Ulaliki
10:30 Kudzipatulila na Ubatizo
11:00 Nyimbo Na. 48
KUMASANA
12:10 Nyimbo Zamalimba
12:20 Nyimbo Na. 63 na Pemphelo
12:30 Nkhani ya Anthu Onse: Imani ku Mbali ya Kulambila Koona
13:00 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:30 Nyimbo Na. 76 na Zilengezo
13:40 Yosiilana: Tengelani Kulimba Mtima kwa Khristu Zinthu Zikavuta . . .
M’banja
Ku Sukulu
Ku Nchito
Kumene Tikhala
14:40 Kulimba Mtima Kwanu ‘Kudzabweletsa Mphoto Yaikulu’
15:15 Nyimbo Na. 119 na Pemphelo