LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 152
  • Malo Amene Adzakubweletselani Citamando

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Malo Amene Adzakubweletselani Citamando
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Tamandani Yehova, Mulungu Wathu!
    Imbirani Yehova
  • Tamandani Yehova, Mulungu Wathu!
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Imbani Nafe Nyimbo ya Ufumu!
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Tiyeni Tiimbe Nyimbo ya Ufumu!
    Imbirani Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 152

NYIMBO 152

Malo Amene Adzakubweletselani Citamando

Yopulinta

(1 Mafumu 8:27; 1 Mbiri 29:14)

  1. 1. Yehova Mulungu Wamphamvu,

    Ndimwe munalenga zonse.

    Inde, ngakhale kumwambako

    Imwe simungakwaneko.

    Maloŵa olambililamo

    Ndipo ni otsangalatsa.

    Timakondwela capamodzi

    Pamene titumikila.

    (BILIJI)

    Zonse tili nazo

    Ndimwe munatipatsa.

    Inde, zonse zimene

    tipeleka n’zanu.

    (KOLASI)

    Zikomo Atate Yehova

    Pa zonse mwaticitila.

    Maloŵa adzabweletsadi

    Citamando kwa inuyo.

  2. 2. Yehova munali kudziŵa

    Zofuna za mtima wathu.

    Mwatipatsa malo abwino

    Okwezela dzina lanu.

    Maloŵa adzathandizila

    Atumiki anu onse

    Kuti aigwiledi nchito

    Yolalikila kwa onse.

    (BILIJI)

    Ise tipeleka

    Nthawi na cuma cathu.

    Ndinu woyeneleladi

    Kutamandiwa.

    (KOLASI)

    Zikomo Atate Yehova

    Pa zonse mwaticitila.

    Maloŵa adzabweletsadi

    Citamando kwa inuyo.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani