Tsiku Laciŵili
“Khalani oleza mtima kwa onse” 1 Atesalonika 5:14
M’maŵa
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 58 na Pemphelo
8:40 YOSIYILANA: “Timasonyeza Kuti Ndife Atumikia Mulungu . . . Mwa Kukhala Oleza Mtima”
• Pamene Tilalikila (Machitidwe 26:29; 2 Akorinto 6:4, 6)
• Potsogoza Maphunzilo a Baibo (Yohane 16:12)
• Polimbikitsana Wina na Mnzake (1 Atesalonika 5:11)
• Mukamatumikila Monga Mkulu (2 Timoteyo 4:2)
9:30 Inu Amene Mwaonetsedwa Kuleza Mtima, Onetsani Kuleza Mtima! (Mateyu 7:1, 2; 18:23-35)
9:50 Nyimbo Na. 138 na Zilengezo
10:00 YOSIYILANA: ‘Moleza Mtima, PitilizaniKulolelana m’Cikondi’
• Acibale Amene si Mboni (Akolose 4:6)
• Mnzanu wa mu Ukwati (Miyambo 19:11)
• Ana Anu (2 Timoteyo 3:14)
• Acibale Odwala Kapena Okalamba (Aheberi 13:16)
10:45 UBATIZO: Kuleza Mtima kwa Yehova Ni Cipulumutso Cathu! (2 Petulo 3:13-15)
11:15 Nyimbo Na. 75 na Zilengezo
Masana
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 106
12:50 Samalani na Mtima Wongofuna KudzisangalatsaNthawi Yomweyo (1 Atesalonika 4:3-5; 1 Yohane 2:17)
13:15 YOSIYILANA: “Woleza Mtima ni WabwinoKuposa Munthu Wodzikuza”
• Tengelani Abele, Osati Adamu (Mlaliki 7:8)
• Tengelani Yakobo, Osati Esau (Aheberi 12:16)
• Tengelani Mose, Osati Kora (Numeri 16:9, 10)
• Tengelani Samueli, Osati Sauli (1 Samueli 15:22)
• Tengelani Yonatani, Osati Abisalomu (1 Samueli 23:16-18)
14:15 Nyimbo Na. 87 na Zilengezo
14:25 SEŴELO: ‘Lola Yehova AkutsogolelePanjila Yako’—Gawo 1 (Salimo 37:5)
14:55 ‘Pozunzidwa, Timapilila Moleza Mtima’ (1 Akorinto 4:12; Aroma 12:14, 21)
15:30 Nyimbo Na. 79 na Pemphelo Lothela