Tsiku Lacitatu
“Yehova azidzayembekezela kuti akukomeleni mtima” Yesaya 30:18
M’maŵa
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 95 na Pemphelo
8:40 YOSIYILANA: Citsanzo ca Kuleza Mtima Cimene Tingatengele—Aneneli
• Eliya (Yakobo 5:10, 17, 18)
• Mika (Mika 7:7)
• Hoseya (Hoseya 3:1)
• Yesaya (Yesaya 7:3)
• Ezekieli (Ezekieli 2:3-5)
• Yeremiya (Yeremiya 15:16)
• Danieli (Danieli 9:22, 23)
10:05 Nyimbo Na. 142 na Zilengezo
10:15 NKHANI YA ANTHU ONSE: Kodi Mulungu Adzacitapo Kanthu Kuti Akuthandizeni? (Yesaya 64:4)
10:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
11:15 Nyimbo Na. 94 na Kupumula
Masana
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 114
12:50 SEŴELO: ‘Lola Yehova Akutsogolele Panjila Yako’—Gawo 2 (Salimo 37:5)
13:30 Nyimbo Na. 115 na Zilengezo
13:40 Yehova Akuyembekezela Moleza Mtima Kuti Akuonetseni Kukoma Mtima (Yesaya 30:18-21; 60:17; 2 Mafumu 6:15-17; Aefeso 1:9, 10)
14:40 Nyimbo Yatsopano na Pemphelo Lothela