UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Khalanibe Okhulupilika Pamene M’bululu Wanu Wacotsedwa
Tambani vidiyo yakuti Muzicilikiza Mokhulupilika Malamulo a Yehova—Pewani Anthu Ocotsedwa , ndiyeno yankhani mafunso aya:
Kodi cikhulupililo ca makolo a Soniya cinaikidwa pa ciyeso motani?
N’ciani cinawathandiza kukhalabe okhulupilika?
Nanga kukhulupilika kwawo kwa Yehova kunam’thandiza bwanji Soniya?