LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsa. 8
  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Nyama

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Nyama
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Analigaŵa Mwanzelu Dziko la Kanani
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Anawamenyela Nkhondo Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambila Motani?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amawadela Nkhawa Akazi
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 July tsa. 8

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Nyama

Nyama imene inali kuvutika anayenela kuithandiza (Deut. 22:4; it-1 375-376)

Mbalame imene inali ndi ana sanayenele kuicitila nkhanza (Deut. 22:6, 7; it-1 621 ¶1)

Nyama zosiyana sanayenele kuzimanga m’goli limodzi (Deut. 22:10; w03 10/15 32 ¶1-2)

Ng’ombe na bulu zamangidwa pa joko imodzi. Joko yapendekela mbali imodzi cifukwa nyamazo n’zosiyana kukula kwake.

Mmene timacitila zinthu na nyama ni nkhani yaikulu kwa Yehova. Sitiyenela kuzicitila nkhanza kapena kuzipha monga cinthu cotisangalatsa.—Miy. 12:10.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani