LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 2
  • Funani Citetezo M’manja a Yehova “Amene Adzakhalapo Mpaka Kale-kale”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Funani Citetezo M’manja a Yehova “Amene Adzakhalapo Mpaka Kale-kale”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amawadela Nkhawa Akazi
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mfundo Zothandiza Kuweluza Milandu Mwacilungamo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambila Motani?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 2
M’bale wacikulille akuŵelenga Baibo, ndipo akuyelekezela m’maganizo mwake kuti akuona gulu lankhondo la Aiguputo litamizidwa m’Nyanja Yofiila.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Funani Citetezo M’manja a Yehova “Amene Adzakhalapo Mpaka Kale-kale”

Yehova amafuna tizikhala na makhalidwe abwino (Deut. 33:26; it-2 51)

Yehova amakhala wokonzeka kuseŵenzetsa mphamvu zake kuti atithandize (Deut. 33:27; rr 120, kabokosi)

Mofanana na Mose, tiyenela kukhulupilila kuti Yehova adzatipulumutsa (Deut. 33:29; w11 9/15 19 ¶16)

Tikakumana na mayeso, Yehova amaticilikiza na manja ake amene adzakhalapo mpaka kale-kale. Amatithandiza tikadwala kapena tikapsinjika maganizo, tikakhala acisoni, kapena pamene tacita colakwa koma talapa.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani