LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsa. 3
  • Timayamika Yehova Cifukwa ca Cikondi Canu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Timayamika Yehova Cifukwa ca Cikondi Canu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • “Khalani Opatsa”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Mphamvu ya ‘Tumakobili Tuŵili Twatung’ono’
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • “Okonzeka Kupeleka Mphatso kwa Yehova”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • ‘Muziika Kenakake Pambali’
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 November tsa. 3
Zithunzi: 1. M’bale akuponya ndalama m’bokosi la zopeleka. 2. JW Box. 3. Abale akuseŵenza pamalo okonzelapo vidiyo.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Timayamika Yehova Cifukwa ca Cikondi Canu

Akhristu a mu mpingo wa ku Tesalonika anaonetsa cikondi kwa Akhristu anzawo, ngakhale kuti nawonso anali kukumana na mavuto. (2 Ates. 1:3, 4) Masiku anonso, anthu a Yehova amaonetsa cikondi ngati cimeneco kwa abale na alongo padziko lonse lapansi. Nkhani za pa jw.org za mutu wakuti “Mmene Zopeleka Zanu Zimagwilila Nchito,” zimaonetsa mmene zopeleka zanu zimathandizila abale m’nthawi zovuta zino. Tikuyamikilani kaamba ka cikondi canu komanso cifukwa ca kucilikiza kwanu mowoloŵa manja.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI “TIMAYAMIKA MULUNGU NTHAWI ZONSE CIFUKWA CA INU,” NDIYENO YANKHANI MAFUNSO AWA:

• Kodi zopeleka zathu zimathandizilanso pa nchito zina ziti?

• Kodi njila yabwino kwambili yopelekela thandizo la ndalama kwa abale na alongo athu osoŵa ni iti?—Onaninso nkhani ya pa jw.org ya mutu wakuti “Zoculuka Zimathandizila pa Zimene Akusoŵa”

PHUNZILANI ZAMBILI PA INTANETI

Kodi mungapange bwanji zopeleka zothandizila pa nchito ya Mboni za Yehova? Dinizani pa linki yakuti “Donations” imene ili m’munsi mwa peji yoyamba ya JW Laibulali. M’maiko ambili, mukaloŵa pamenepo mudzapezapo linki ya nkhani yakuti “Frequently Asked Questions” (FAQ), imene imayankha mafunso amene anthu amafunsa kaŵili-kaŵili pankhani yopanga zopeleka.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani