LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsa. 3
  • “Khalani Opatsa”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Khalani Opatsa”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Timayamika Yehova Cifukwa ca Cikondi Canu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • ‘Muziika Kenakake Pambali’
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Mphamvu ya ‘Tumakobili Tuŵili Twatung’ono’
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • “Okonzeka Kupeleka Mphatso kwa Yehova”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 November tsa. 3
Mlongo wacikulile akuseŵenzetsa tabuleti popanga copeleka kupitila pa Intaneti. Zithunzi: Mmene zopeleka zathu zimagwilila nchito. 1. Kupulinta mabuku ku Beteli. 2. Masukulu a utumiki. 3. Ulaliki wapoyela. 4. Nchito zomanga.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

“Khalani Opatsa”

Yesu anaonetsa kuti kuwoloŵa manja ni khalidwe limene tingatengele kwa ena. (Luka 6:38) Khalidwe lanu la kupatsa limasonkhezela abale na alongo anu kukhala okoma mtima komanso owoloŵa manja.

Kupatsa mowoloŵa manja ni mbali ya kulambila kwathu. Tikakhala owoloŵa manja komanso tikamathandiza Akhristu anzathu amene afunika thandizo, Yehova amaona ndipo analonjeza kuti adzatifupa.—Miy. 19:17.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI TIMAYAMIKILA KHALIDWE LANU LA KUPATSA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Kodi zopeleka zanu zimagwilitsidwa nchito motani pothandiza abale na alongo athu?

  • Kaya zopeleka zathu zimakhala zoculuka kapena zocepa, n’cifukwa ciyani sitiyenela kuleka kukhala opatsa?—Onaninso nkhani ya pa jw.org yakuti “Zoculuka Zimathandizila pa Zimene Zikusoŵa.”

PHUNZILANI ZAMBILI PA INTANETI

Kodi mungapange bwanji zopeleka zothandizila pa nchito ya Mboni za Yehova? Dinizani pa linki yakuti “Donations,” imene ili m’munsi mwa tsamba loyamba la JW Laibulale®. M’maiko ambili, mukaloŵa pamenepo mudzapeza polemba kuti FAQ, pamene pali linki ya dokyumenti yakuti Donations to Jehovah’s Witnesses—Frequently Asked Questions.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani