LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsa. 3
  • ‘Muziika Kenakake Pambali’

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • ‘Muziika Kenakake Pambali’
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • “Khalani Opatsa”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Timayamika Yehova Cifukwa ca Cikondi Canu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mphamvu ya ‘Tumakobili Tuŵili Twatung’ono’
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • “Okonzeka Kupeleka Mphatso kwa Yehova”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 November tsa. 3
Mlongo wacikulile akuponya ndalama m’bokosi la zopeleka m’Nyumba ya Ufumu. Zithunzi: 1. Abale na alongo akuthandiza pa nchito yomanga. 2. Pulogilamu ya JW Broadcasting. 3. Abale na alongo akutsitsa zinthu mu thilaki.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

‘Muziika Kenakake Pambali’

Tiyenela kucita zopeleka mwaufulu nthawi zonse. Izi n’zimene mtumwi Paulo anatilimbikitsa kucita pamene anati, ‘muziika kenakake pambali.’ (1 Akor. 16:2) Kutsatila malangizo ouzilidwa amenewa kumatithandiza kupititsa patsogolo kulambila koyela, ndipo kumatibweletsela cimwemwe. Mwina tingaone kuti zopeleka zathu n’zocepa kwambili. Koma Yehova amayamikila ngako kuona kuti ndife ofunitsitsa kumulemekeza na zinthu zathu zamtengo wapatali.—Miy. 3:9.

TAMBANI VIDIYO YAKUTI TIKUYAMIKILANI CIFUKWA COIKA KENAKAKE PAMBALI, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATILAWA:

  • Kodi pamakhala mapindu otani tikamakonzelatu zopeleka zathu?

  • Kodi ena amacita ciyani kuti ‘aziika kenakake pambali’?

PHUNZILANI ZAMBILI PA INTANETI

Cizindikilo ca “Zopeleka“, coonetsa dzanja lanyamula ka kobili.

Kodi mungapange bwanji zopeleka zothandizila pa nchito ya Mboni za Yehova? Dinizani pa linki yakuti “Donations,” imene ili m’munsi mwa tsamba loyamba la JW Laibulale®. M’maiko ambili, mukaloŵa pamenepo mudzapeza polemba kuti FAQ, pomwe pali linki ya dokyumenti yakuti Donations to Jehovah’s Witnesses—Frequently Asked Questions.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani