LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 9
  • Funsilani Kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Funsilani Kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Malo Amene Amalemekeza Mlangizi Wathu Wamkulu
    Mmene Zopeleka Zanu Zimagwilila Nchito
  • Kodi Mungakonde Kufunsila Kuti Mukaloŵe Sukulu ya Alengezi a Ufumu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Pitilizani Kulandila Maphunzilo Aumulungu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Kodi Apainiya Amalandila Maphunzilo Anji?
    Ndani Amene Akucita Cifunilo Ca Yehova Masiku Ano?
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 9

UMOYO WATHU WACIKHRISTU | DZIIKILENI ZOLINGA ZA CAKA CA UTUMIKI CATSOPANO

Funsilani Kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu

Kuti mufunsile kukaloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu (SKE), musacite kuyembekezela mpaka zinthu zikakhale bwino kwambili pa umoyo wanu. Cofunikila kwenikweni ni kukhala munthu wauzimu, komanso wofunitsitsa kulandila utumiki uliwonse umene mungapatsidwe m’gulu la Yehova.—Yes. 6:8.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI LOŴANI PA KHOMO LA ZOCITA ZAMBILI M’CIKHULUPILILO—FUNSILANI KULOŴA SUKULU YA ALENGEZI A UFUMU, KENAKO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Cithunzi coonetsa zocitika za m’vidiyo yakuti “Loŵani pa Khomo la Zocita Zambili M’cikhulupililo—Funsilani Kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu.” Gabriel akusinkhasinkha mmene Yehova wamudalitsila.

    N’cifukwa ciyani Gabriel anali kukayikila zofunsila kuti akaloŵe Sukulu ya Alengezi a Ufumu? Nanga analimbikitsidwa bwanji atasinkhasinkha mfundo ya pa Afilipi 4:13?

Ngati colinga canu ni kukaloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu, kambani na akulu a mumpingo wanu. Iwo angakambilane nanu ziyenelezo zofunikila kuti mufunsile kukaloŵa sukuluyi.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani