CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Pewani Zinthu Zopanda Pake
Maso anacititsa Akani kutenga zinthu zisali zake (Yos. 7:1, 20, 21; w10 4/15 20 ¶5)
Zocita za Akani zinabweletsa mavuto pa banja lake na ku mtundu wonse wa Isiraeli (Yos. 7:4, 5, 24-26; w97 8/15 28 ¶2)
Tiyenela kukhala odziletsa (1 Yoh. 2:15-17; w10 4/15 21 ¶8)
Tizipewa zinthu zopanda pake, zimene sizidzakhalamo m’dziko latsopano la Mulungu lolungama.—2 Pet. 3:13.