Numeri 31:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: 2 “Uwabwezere+ Amidiyani chifukwa cha zimene anachitira Aisiraeli.+ Pambuyo pake udzaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ako.”*+
31 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: 2 “Uwabwezere+ Amidiyani chifukwa cha zimene anachitira Aisiraeli.+ Pambuyo pake udzaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ako.”*+