Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 14:4-6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 mudzanena mwambi uwu wonyoza mfumu ya Babulo:

      “Amene ankagwiritsa ntchito anzake mokakamiza uja wawonongedwa!

      Kuponderezedwa kuja kwatha ndithu!+

       5 Yehova wathyola ndodo ya anthu oipa,

      Ndodo ya anthu olamulira.+

       6 Wathyola ndodo ya amene ankakwapula mwaukali komanso mosalekeza anthu a mitundu ina,+

      Amene anagonjetsa mitundu ya anthu mokwiya powazunza mosalekeza.+

  • Yesaya 47:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+

      Ndinalola kuti cholowa changa chidetsedwe+

      Ndipo ndinawapereka mʼmanja mwako.+

      Koma iwe sunawachitire chifundo.+

      Ngakhale munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+

  • Yeremiya 30:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Choncho onse okuwononga adzawonongedwa,+

      Ndipo adani ako onse nawonso adzatengedwa kupita ku ukapolo.+

      Amene akulanda katundu wako nawonso adzalandidwa katundu wawo.

      Ndipo anthu onse amene akulanda zinthu zako ndidzawapereka mʼmanja mwa olanda zinthu.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani