CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Muzilola Kuti Yehova Azikugwiritsani Ntchito
[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Ezara.]
Yehova analimbikitsa mtima wa Mfumu Koresi kuti akamasule Aisiraeli (Eza 1:1-3; w22.03 12:1)
Yehova analimbikitsa mtima wa anthu ake kuti akamangenso kachisi (Eza 1:5; w17.10 4:2)
Ngati mungadzipereke, Yehova akhoza kuchititsa kuti mukhale chilichonse chimene iye akufuna kuti akwaniritse cholinga chake.