Levitiko 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Pamenepo ndidzakucheukirani,+ kukuchititsani kubereka ana ambiri ndi kukuchulukitsani.+ Ndipo ndidzasunga pangano langa ndi inu.+ Salimo 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ananditenga ndi kundiika pamalo otakasuka.+Anandipulumutsa chifukwa anakondwera nane.+ Salimo 118:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’masautso anga ndinaitana Ya.+Ya anandiyankha ndi kundiika pamalo otakasuka.+
9 “‘Pamenepo ndidzakucheukirani,+ kukuchititsani kubereka ana ambiri ndi kukuchulukitsani.+ Ndipo ndidzasunga pangano langa ndi inu.+