Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Salimo 107:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo.+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+ Salimo 120:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 120 Ndinafuulira Yehova m’masautso anga,+Ndipo iye anandiyankha.+
19 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo.+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+