Deuteronomo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Chidzadalitsika chipatso cha mimba yako,+ chipatso cha m’dziko lanu, chipatso cha ziweto zako,+ ana a ng’ombe zako ndi ana a nkhosa zako.+ Nehemiya 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo munawachulukitsira ana awo ngati nyenyezi zakumwamba.+ Mutatero munawalowetsa m’dziko+ limene munalonjeza makolo awo+ kuti akalowe ndi kulitenga. Salimo 107:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mulungu amawadalitsa moti amachuluka kwambiri,+Ndipo salola kuti ng’ombe zawo zikhale zochepa.+
4 “Chidzadalitsika chipatso cha mimba yako,+ chipatso cha m’dziko lanu, chipatso cha ziweto zako,+ ana a ng’ombe zako ndi ana a nkhosa zako.+
23 Ndipo munawachulukitsira ana awo ngati nyenyezi zakumwamba.+ Mutatero munawalowetsa m’dziko+ limene munalonjeza makolo awo+ kuti akalowe ndi kulitenga.