2 Esau anatenga akazi pakati pa ana aakazi a ku Kanani.+ Anatenga Ada,+ mwana wamkazi wa Eloni, Mhiti.+ Anatenganso Oholibama,+ yemwe anali mwana wamkazi wa Ana, komanso anali mdzukulu wa Zibeoni, Mhivi.
3 Usadzachite nawo mgwirizano wa ukwati. Usadzapereke ana ako aakazi kwa ana awo aamuna ndipo usadzatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana ako aamuna.+