Yesaya 65:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Mmbulu+ ndi mwana wa nkhosa zidzadyera pamodzi.+ Mkango udzadya udzu ngati ng’ombe yamphongo,+ ndipo njoka izidzadya fumbi.+ Zimenezi sizidzapweteka aliyense+ kapena kuwononga chilichonse m’phiri langa lonse loyera,”+ watero Yehova. Mika 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Adzanyambita fumbi ngati njoka.+ Adzatuluka m’malo awo obisalamo+ ngati zokwawa zapadziko lapansi ali ndi mantha. Adzabwera kwa Yehova Mulungu akunjenjemera ndipo adzachita nanu mantha.”+
25 “Mmbulu+ ndi mwana wa nkhosa zidzadyera pamodzi.+ Mkango udzadya udzu ngati ng’ombe yamphongo,+ ndipo njoka izidzadya fumbi.+ Zimenezi sizidzapweteka aliyense+ kapena kuwononga chilichonse m’phiri langa lonse loyera,”+ watero Yehova.
17 Adzanyambita fumbi ngati njoka.+ Adzatuluka m’malo awo obisalamo+ ngati zokwawa zapadziko lapansi ali ndi mantha. Adzabwera kwa Yehova Mulungu akunjenjemera ndipo adzachita nanu mantha.”+