Miyambo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwana wanga, tamvera malangizo a bambo ako,+ ndipo usasiye malamulo a mayi ako,+ Akolose 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ananu, muzimvera+ makolo anu pa zinthu zonse, pakuti kuchita zimenezi kumakondweretsa Ambuye.