Genesis 27:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Tsopano, tamvera zimene ndikuuze mwana wanga.+ Nyamuka, thawira kwa Labani mlongo wanga, ku Harana.+ Machitidwe 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+
43 Tsopano, tamvera zimene ndikuuze mwana wanga.+ Nyamuka, thawira kwa Labani mlongo wanga, ku Harana.+
2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+