Genesis 48:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo anadalitsa Yosefe,+ kuti: “Mulungu woona amene makolo anga Abulahamu ndi Isaki anayenda pamaso pake,+Mulungu woona amene wakhala m’busa wanga moyo wanga wonse mpaka lero,+
15 Pamenepo anadalitsa Yosefe,+ kuti: “Mulungu woona amene makolo anga Abulahamu ndi Isaki anayenda pamaso pake,+Mulungu woona amene wakhala m’busa wanga moyo wanga wonse mpaka lero,+