Levitiko 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Ngati mkazi akukha ndipo zimene akukhazo ndi magazi,+ azikhala masiku 7 ali wodetsedwa+ chifukwa cha kusamba+ kwakeko, ndipo aliyense womukhudza azikhala wodetsedwa kufikira madzulo. Ezekieli 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu avula bambo awo.+ Iwo agona ndi mkazi wodetsedwa amene akusamba.+
19 “‘Ngati mkazi akukha ndipo zimene akukhazo ndi magazi,+ azikhala masiku 7 ali wodetsedwa+ chifukwa cha kusamba+ kwakeko, ndipo aliyense womukhudza azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.