Genesis 27:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Tsopano, tamvera zimene ndikuuze mwana wanga.+ Nyamuka, thawira kwa Labani mlongo wanga, ku Harana.+ Genesis 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nyamuka, pita ku Padana-ramu kunyumba ya Betuele bambo a mayi ako. Kumeneko ukatenge mkazi pakati pa ana a Labani mlongo wa mayi ako.+
43 Tsopano, tamvera zimene ndikuuze mwana wanga.+ Nyamuka, thawira kwa Labani mlongo wanga, ku Harana.+
2 Nyamuka, pita ku Padana-ramu kunyumba ya Betuele bambo a mayi ako. Kumeneko ukatenge mkazi pakati pa ana a Labani mlongo wa mayi ako.+