Genesis 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Esau anafunsa kuti: “Nanga n’chifukwa chiyani watumiza khamu lonse limene ndakumana nalo lija?”+ Poyankha iye anati: “Ndachita zimenezi kuti mundikomere mtima mbuyanga.”+ Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+
8 Tsopano Esau anafunsa kuti: “Nanga n’chifukwa chiyani watumiza khamu lonse limene ndakumana nalo lija?”+ Poyankha iye anati: “Ndachita zimenezi kuti mundikomere mtima mbuyanga.”+
16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+